Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 19:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

m'mene mukonda awo akudana nanu, ndi kudana nao amene akukondani. Pakuti lero mwalalikira kuti simusamalira konse akalonga ndi anyamata; pakuti lero ndizindikira kuti tikadafa ife tonse, ndipo akadakhala ndi moyo Abisalomu, pamenepo mukadakondwera ndithu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 19

Onani 2 Samueli 19:6 nkhani