Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 19:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace tsono nyamukani, muturuke, nimulankhule zowakondweretsa anyamata anu; pakuti ndilumbira, Pali Yehova, kuti mukapanda kuturuka inu, palibe munthu mmodzi adzakhala nanu usiku uno; ndipo cimeneci cidzakuipirani koposa zoipa zonse zinakugwerani kuyambira ubwana wanu kufikira tsopanoli.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 19

Onani 2 Samueli 19:7 nkhani