Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 19:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoabu anafika ku nyumba ya mfumu, nati, Lero mwacititsa manyazi nkhope zao za anyamata anu onse, amene anapulumutsa moyo wanu lero, ndi miyoyo ya ana anu amuna ndi akazi, ndi miyoyo ya akazi anu, ndi miyoyo ya akazi anu ang'ono;

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 19

Onani 2 Samueli 19:5 nkhani