Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 3:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati Yehosafati, Mau a Yehova ali ndi iyeyo, Pamenepo mfumu ya Israyeli, ndi Yehosafati, ndi mfumu ya Edomu, anatsikira kuli iye.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 3

Onani 2 Mafumu 3:12 nkhani