Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 3:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Yehosafati anati, Palibe pano mneneri wa Yehova kodi, kuti tifunsire Yehova mwa iye? Ndipo wina wa anyamata a mfumu ya Israyeli anayankha, nati, Elisa mwana wa Safati ali pano, ndiye uja anathira madzi m'manja a Eliya.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 3

Onani 2 Mafumu 3:11 nkhani