Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 3:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Elisa anati kwamfumuya Israyeli, Ndiri ndi ciani ndi inu? mukani kwa aneneri a atate wanu, ndi kwa aneneri a amai wanu. Koma mfumu ya Israyeli inanena naye, Iai, pakuti Yehova anaitana mafumu ife atatu kutipereka m'dzanja la Moabu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 3

Onani 2 Mafumu 3:13 nkhani