Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 28:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumuvo inanena naye, Usaope, kodi ulikuona ciani? Mkaziyo nanena ndi Sauli, Ndirikuona milungu irikukwera kuturuka m'kati mwa dziko.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 28

Onani 1 Samueli 28:13 nkhani