Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 28:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mkaziyo pakuona Samueli, anapfuula ndi mau akuru; ndi mkaziyo analankhula ndi Sauli, nati, Munandinyengeranji? popeza inu ndinu Sauli.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 28

Onani 1 Samueli 28:12 nkhani