Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 5:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsono, lamulirani kuti anditemere mitengo yamkungudza ku Lebano, ndipo akapolo anga adzakhala ndi akapolo anu, ndipo ndidzakupatsani mphotho ya akapolo anu monga mudzanena; popeza mudziwa kuti pakati pa ife palibe mmisiri wakudziwa kutema mitengo ngati anthu a ku Sidoni.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 5

Onani 1 Mafumu 5:6 nkhani