Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 5:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo taonani, ndikuti ndimangire dzina la Yehova Mulungu wanga nyumba, monga Yehova anauza atate wanga Davide, ndi kuti, Mwana wako ndidzamuika pa mpando wako wacifumu m'malo mwako, iyeyo adzamangira dzina langa nyumbayo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 5

Onani 1 Mafumu 5:5 nkhani