Yuda watengedwa ndende cifukwa ca msauko ndi ukapolo waukuru;Akhala mwa amitundu, sapeza popuma;Onse akumlondola anampeza pakati popsinjikiza.