Uliralira usiku; misozi yace iri pa masaya ace;Mwa onse amene anaukonda mulibe mmodzi wakuutonthoza:Mabwenzi ace onse aucitira ziwembu,Asanduka adani ace.