Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Maliro 1:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

M'njira za Ziyoni mulira posoweka akudzera msonkhano;Pa zipata zace zonse papasuka; ansembe ace onse ausa moyo;Anamwali ace asautsidwa; iye mwini namva zowawa.

Werengani mutu wathunthu Maliro 1

Onani Maliro 1:4 nkhani