Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yuda 1:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Okondedwa, pakucira cangu conse cakukulemberani za cipulumutso ca ife tonse, ndafulumidwa mtima ine kukulemberani ndi kudandaulira kuti mulimbanetu cifukwa ca cikhulupiriro capatsidwa kamodzi kwa oyera mtima.

Werengani mutu wathunthu Yuda 1

Onani Yuda 1:3 nkhani