Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yuda 1:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti pali anthu ena anakwawira m'tseri, ndiwo amene aja adalembedwa maina ao kale, kukalandira citsutso ici, anthu osapembedza, akusandutsa cisomo ca Mulungu wathu cikhale cilak olako conyansa, nakaniza Mfumu wayekha, ndi Ambuye wathu, Yesu Kristu.

Werengani mutu wathunthu Yuda 1

Onani Yuda 1:4 nkhani