Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Marko 8:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anadziitanira khamulo la anthu pamodzi ndi ophunzira ace, nati kwa iwo, Ngati munthu afuna kudza pambuyo panga, adzikanize yekha, nanyamule mtanda wace, nanditsate Ine.

Werengani mutu wathunthu Marko 8

Onani Marko 8:34 nkhani