Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Marko 8:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti yense wakufuna kupulumutsa moyo wace adzautaya; ndipo yense wakutaya moyo wace cifukwa ca Ine, ndi cifukwa ca Uthenga Wabwino, adzaupulumutsa.

Werengani mutu wathunthu Marko 8

Onani Marko 8:35 nkhani