Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Marko 6:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Si mmisiri wa mitengo uyu, mwana wa Mariya, mbale wao wa Yakobo, ndi Yose, ndi Yuda, ndi Simoni? Ndipo alongo ace sali nafe pano kodi? Ndipo anakhumudwa ndi Iye.

Werengani mutu wathunthu Marko 6

Onani Marko 6:3 nkhani