Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Marko 6:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo Iye anaturuka kumeneko; nafika ku dziko la kwao; ndipo ophunzira ace anamtsata.

2. Ndipo pofika dzuwa la Sabata, anayamba kuphunzitsa m'sunagoge; ndipo ambiri anamva Iye, nazizwa, nanena, Uyu adazitenga kuti izi? Nzeru yopatsidwa kwa munthuyu njotani, ndi zamphamvu zotere zocitidwa ndi manja ace?

3. Si mmisiri wa mitengo uyu, mwana wa Mariya, mbale wao wa Yakobo, ndi Yose, ndi Yuda, ndi Simoni? Ndipo alongo ace sali nafe pano kodi? Ndipo anakhumudwa ndi Iye.

Werengani mutu wathunthu Marko 6