Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 4:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'mene adapemphera iwo, panagwedezeka pamalo pamene adasonkhanirapo; ndipo anadzazidwa onse ndi Mzimu Woyera, nalankhula mau a Mulungu molimbika mtima.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 4

Onani Macitidwe 4:31 nkhani