Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 4:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo unyinji wa iwo akukhulupira anali wa mtima umodzi ndi moyo umodzi; ndipo sananena mmodzi kuti kanthu ka cuma anali naco ndi kace ka iye yekha; koma anali nazo zonse zodyerana.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 4

Onani Macitidwe 4:32 nkhani