Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 9:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma dzuwa lidapendeka; ndipo khumi ndi awiriwo anadza, nati kwa iye, Tauzani makamu a anthu amuke, kuti apite ku midzi yoyandikira ndi kumiraga, kukafuna pogona, ndi kupeza zakudya; cifukwa tiri ku malo acipululu kuno.

Werengani mutu wathunthu Luka 9

Onani Luka 9:12 nkhani