Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 8:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo za pathanthwe ndiwo amene, pakumva, alandira mau ndi kukondwera; koma alibe mizu; akhulupirira kanthawi, ndipo pa nthawi ya mayesedwe angopatuka.

Werengani mutu wathunthu Luka 8

Onani Luka 8:13 nkhani