Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 4:40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pakulowa dzuwa anthu onse amene anali nao odwala ndi nthenda za mitundu mitundu, anadza nao kwa iye; ndipo iye anaika manja ace pa munthu ali yense wa iwo, nawaciritsa.

Werengani mutu wathunthu Luka 4

Onani Luka 4:40 nkhani