Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 12:54 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma iye ananenanso kwa makamu a anthu, 7 Pamene pali ponse muona mtambo wokwera kumadzulo, pomwepo munena, kuti, Ikudza mvula; ndipo itero.

Werengani mutu wathunthu Luka 12

Onani Luka 12:54 nkhani