Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 12:53 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Adzatsutsana atate ndi mwana wace, ndi mwana ndi atate wace; amace adzatsutsana ndi mwana wamkazi'l ndi mwana wamkazi ndi amace, mpongozi adzatsutsana ndi mkazi wa mwana wace, ndi mkaziyo ndi mpongozi wace.

Werengani mutu wathunthu Luka 12

Onani Luka 12:53 nkhani