Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 9:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anatsegula pa dzenje la phompho; ndipo unakwera utsi woturuka m'dzenjemo, ngati utsi wa ng'anjo yaikuru; ndipo dzuwa ndi thambo zinada, cifukwa ca utsiwo wa kudzenje,

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 9

Onani Cibvumbulutso 9:2 nkhani