Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 9:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mngelo wacisanu anaomba, ndipo ndinaona nyenyezi yocokera kumwamba idagwa padziko; ndipo anampatsa iye cifunguliro ca dzenje la phompho.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 9

Onani Cibvumbulutso 9:1 nkhani