Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 8:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mngelo waciwiri anaomba, ndipo monga ngati phiri lalikuru lakupserera ndi mota Iinaponyedwa m'nyanja; ndipo limodzi la magawo atatu a nyanja linasanduka mwazi;

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 8

Onani Cibvumbulutso 8:8 nkhani