Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 8:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo woyamba anaomba, ndipo panakhala matalala ndi moto, zosanganiza ndi mwazi, ndipo anazitaya pa dziko lapansi; ndipo limodzi la magawo atatu a dziko lidapserera, ndipo limodzi la magawo atatu a mitengo lidapserera, ndipo msipu wonse udapserera.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 8

Onani Cibvumbulutso 8:7 nkhani