Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 8:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mngelo wacinai anaomba, ndipo limodzi la magawo atatu a dzuwa linagwidwa, ndi limodzi la magawo atatu a mwezi, ndi limodzi la magawo atatu a nyenyezi; kuti limodzi la magawo ao atatu lidetsedwe, ndi kuti limodzi la magawo ace atatu a usana lisawale, ndi usiku momwemo.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 8

Onani Cibvumbulutso 8:12 nkhani