Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 21:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mzinda ukhala wampwamphwa; utali wace ulingana ndi kupingasa kwace: ndipo anayesa mzinda ndi bangolo, mastadiya zikwi khumi ndi ziwiri; utali wace, ndi kupingasa kwace, ndi kutalika kwace zilingana.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 21

Onani Cibvumbulutso 21:16 nkhani