Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 21:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye wakulankhula ridi ine anali nao muyeso, bango lagolidi, kuti akayese mzindawo, ndi zipata zace, ndi linga lace.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 21

Onani Cibvumbulutso 21:15 nkhani