Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 19:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ananena ndi ine, Lemba, Odala iwo amene aitanidwa ku phwando la ukwati wa Mwanawankhosa. Ndipo ananena ndi ine, Iwo ndiwo mau oona a Mulungu.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 19

Onani Cibvumbulutso 19:9 nkhani