Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 19:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinagwa pa mapazi ace kumlambira iye. Ndipo ananena ndi ine, Tapenya, usatero; ine ndine kapolo mnzako, ndi mnzao wa abale ako akukhala nao umboni wa Yesu; lambira Mulungu: pakuti umboni wa Yesu ndiwo Mzimu wa cinenero.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 19

Onani Cibvumbulutso 19:10 nkhani