Ndipo 4 ndinaona ciromboco, ndi mafumu a dziko, ndi magulu a nkhondo ao, osonkhanidwa kucita nkhondo pa iye wakukwera pa kavalo, ndi gulu la nkhondo lace.