Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 19:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo 5 cinagwidwa ciromboco, ndi pamodzi naco mneneri wonyenga amene adacita zizindikilo pamaso pace, zimene anasokeretsa nazo iwo amene adalandira lemba la cirombo, ndi iwo akulambira fano lace; 6 iwo awiri anaponyedwa ali moyo m'nyanja yamoto yakutentha ndi sulfure:

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 19

Onani Cibvumbulutso 19:20 nkhani