Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 19:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuti 3 mudzadye nyama ya mafumu, ndi nyama ya akapitao, ndi nyama ya anthu amphamvu, ndi nyama ya akavalo, ndi ya iwo akukwerapo, ndi nyama ya anthu onse, mfulu ndi akapolo, ndi ang'ono ndi akuru.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 19

Onani Cibvumbulutso 19:18 nkhani