Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 19:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinaona mngelo alikuima m'dzuwa; ndipo anapfuula ndi mau akuru alrunena 1 ndi mbalame zonse zakuuluka pakati pa mlengalenga: 2 Idzani kuno, sonkhanani ku phwando la Mulungu wamkuru,

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 19

Onani Cibvumbulutso 19:17 nkhani