Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 11:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akulu makumi awiri mphambu anai akukhala pamaso pa Mulungu pa mipando yacifumu yao, anagwa nkhope yao pansi nalambira Mulungu,

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 11

Onani Cibvumbulutso 11:16 nkhani