Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 11:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mngelo wacisanu ndi ciwiri anaomba, ndipo panakhala mau akulu m'Mwamba, ndi kunena, Ufumu wa dziko lapansi wayamba kukhala wa Ambuye wathu, ndi wa Kristu wace: ndipo adzacita ufumu kufikira nthawi za nthawi.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 11

Onani Cibvumbulutso 11:15 nkhani