Koma ine nditi, Sanamva iwo kodi! Indetu,Liu lao linaturukira ku dziko lonse lapansi,Ndi maneno ao ku malekezero a dziko lokhalamo anthu.