Koma nditi, Kodi Israyeli alibe kudziwa? Poyamba Mose anena,Ine ndidzacititsa inu nsanje ndi iwo amene sakhala mtundu wa anthu,Ndidzakwiyitsa inu ndi mtundu wopulukira.