Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Atesalonika 1:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kotero kuti ife tokha tidzitamandira za inu m'Mipingo ya Mulungu, cifukwa ca cipiriro canu, ndi cikhulupiriro canu, m'mazunzo anu onse ndi zisautsozo muzimva;

Werengani mutu wathunthu 2 Atesalonika 1

Onani 2 Atesalonika 1:4 nkhani