Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Atesalonika 1:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tiziyamika Mulungu nthawi zonse cifukwa ca inu, abale, monga kuyenera; pakuti cikhulupiriro canu cikula cikulire, ndipo cicurukira cikondanoca inu nonse, yense pa mnzace;

Werengani mutu wathunthu 2 Atesalonika 1

Onani 2 Atesalonika 1:3 nkhani