Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Atesalonika 1:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti iwo okha alalikira za ife, malowedwe athu a kwa inu anali otani; ndi kuti munatembeoukira kwa Mulungu posiyana nao mafano, kutumikira Mulungu weni weni wamoyo,

Werengani mutu wathunthu 1 Atesalonika 1

Onani 1 Atesalonika 1:9 nkhani