Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Zefaniya 3:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndaononga amitundu; nsanja zao za kungondya nza bwinja, ndapasula miseu yao, palibe wopitapo; midzi yao yaonongeka, palibe munthu, palibe wokhalamo.

Werengani mutu wathunthu Zefaniya 3

Onani Zefaniya 3:6 nkhani