Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Zefaniya 3:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndinati, Zedi udzandiopa Ine, udzalola kulangizidwa, kuti pokhala pace pasaonongeke, monga mwa zonse ndamuikira; koma analawirira mamawa, nabvunditsa macitidwe ao onse.

Werengani mutu wathunthu Zefaniya 3

Onani Zefaniya 3:7 nkhani