Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Zefaniya 1:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ngakhale siliva wao, ngakhale golidi wao sizidzakhoza kuwalanditsa tsiku la mkwiyo wa Yehova; koma dziko lonse lidzatha ndi moto wa nsanje yace; pakuti adzacita cakutsiriza, mofulumira, onse okhala m'dziko.

Werengani mutu wathunthu Zefaniya 1

Onani Zefaniya 1:18 nkhani