Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Zefaniya 1:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzatengera anthu zowapsinja, kuti adzayenda ngati anthu a'khungu, popeza anacimwira Yehova; ndi mwazi wao udzatsanulidwa ngati pfumbi, ndi nyama yao idzanga ndowe.

Werengani mutu wathunthu Zefaniya 1

Onani Zefaniya 1:17 nkhani